Psalms 84:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Chauta ndiye dzuŵa ndi chishango, amatichitira chifundo ndi kutipatsa ulemu. Chauta saŵamana zabwino anthu oyenda molungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova Mulungu ndiye dzuwa ndi chikopa; Yehova adzapatsa chifundo ndi ulemerero; sadzakaniza chokoma iwo akuyenda angwiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa ndi chishango; Yehova amapereka chisomo ndi ulemu; Iye sawamana zinthu zabwino iwo amene amayenda mwangwiro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova Mulungu ndiye dzuwa ndi cikopa; Yehova adzapatsa cifundo ndi ulemerero; Sadzakaniza cokoma iwo akuyenda angwiro,