Psalms 84:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta Wamphamvuzonse, ngwodala munthu woika chikhulupiriro chake pa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova wa makamu, wodala munthu wakukhulupirira Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova Wamphamvuzonse, wodala ndi munthu amene amakhulupirira Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova wa makamu, Wodala munthu wakukhulupirira Inu.