Psalms 84:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga ukulakalaka, mpaka kukomoka, kufunitsitsa kuwona mabwalo a Chauta. Inu Mulungu wamoyo, ndikukuimbirani mwachimwemwe ndi mtima wanga wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wanga ulakalaka, inde ukomokanso ndi kufuna mabwalo a Yehova; mtima wanga ndi thupi langa zifuulira kwa Mulungu wamoyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Moyo wanga ukulakalaka, mpaka kukomoka, kufuna mabwalo a Yehova; Mtima wanga ndi thupi langa zikufuwulira Mulungu wamoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wanga ulakalaka, inde ukomokanso ndi kufuna mabwalo a Yehova; Mtima wanga ndi thupi langa zipfuulira kwa Mulungu wamoyo.