Psalms 84:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngodala anthu amene amakhala m'Nyumba mwanu, namaimba nyimbo zotamanda Inu nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Odala iwo akugonera m'nyumba mwanu; akulemekezani chilemekezere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Odala amene amakhala mʼNyumba yanu; nthawi zonse amakutamandani. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Odala iwo akugonera m'nyumba mwanu; Akulemekezani cilemekezere,