Psalms 84:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngodala anthu amene mphamvu zao nzochokera kwa Inu, amene m'mitima mwao amafunitsitsa kudzera m'miseu yopita ku Ziyoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala munthu amene mphamvu yake ili mwa Inu; mumtima mwake muli makwalala a ku Ziyoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Odala amene mphamvu yawo ili mwa Inu, mitima yawo ikufunitsitsa kuyenda mʼmisewu yopita ku Ziyoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala munthu amene mphamvu yace iri mwa Inu; Mumtima mwace muli makwalala a ku Ziyoni,