Psalms 84:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mphamvu zao zimanka zichulukirachulukira. Mulungu wa milungu adzaoneka m'Ziyoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apita mwamphamvu naonjezapo mphamvu, aoneka pamaso pa Mulungu m'Ziyoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amanka nakulirakulira mphamvu mpaka aliyense ataonekera pamaso pa Mulungu mu Ziyoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apita mwamphamvu naonjezapo mphamvu, Aoneka pamaso pa Mulungu m'Ziyoni.