Psalms 84:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, ndinu chishango chathu, yang'anani nkhope ya wodzozedwa wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onani, Mulungu, ndinu chikopa chathu; ndipo penyani pa nkhope ya Wodzozedwa wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yangʼanani chishango chathu, Inu Mulungu; yangʼanani mokoma mtima pa wodzozedwa wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onani, Mulungu, ndinu cikopa cathu; Ndipo penyani pa nkhope ya Wodzozedwa wanu.