Psalms 85:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ake adzakhala okhulupirika pansi pano, ndipo Mulungu wakumwamba adzaŵalungamitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Choonadi chiphukira m'dziko; ndi chilungamo chasuzumira chili m'mwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kukhulupirika kumatumphuka kuchokera ku dziko lapansi, ndipo chilungamo chimayangʼana pansi kuchokera kumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Coonadi ciphukira m'dziko; Ndi cilungamo casuzumira ciri m'mwamba.