Psalms 85:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudaleka ndithu ukali wanu woopsa, mudaletsa mkwiyo wanu woyaka moto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munabweza kuzaza kwanu konse; munabwerera kumkwiyo wanu wotentha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munayika pambali ukali wanu wonse ndi kutembenuka kuchoka ku mkwiyo wanu woopsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munabweza kuzaza kwanu konse; Munabwerera ku mkwiyo wanu wotentha.