Psalms 85:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi simudzatipatsanso moyo, kuti ife anthu anu tikondwere mwa Inu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi simudzatipatsanso moyo, kuti anthu anu akondwerere ndi Inu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi simudzatitsitsimutsanso, kuti anthu anu asangalale mwa Inu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi simudzatipatsanso moyo, Kuti anthu anu akondwerere ndi Inu?