Psalms 85:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, Mulungu ali wokonzekera kuti apulumutse amene amamuwopa, kuti ulemerero wake ukhale m'dziko lathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Indedi chipulumutso chake chili pafupi ndi iwo akumuopa Iye; kuti m'dziko mwathu mukhale ulemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithu chipulumutso chake chili pafupi ndi iwo amene amaopa Iye, kuti ulemerero wake ukhale mʼdziko lathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Indedi cipulumutso cace ciri pafupi ndi iwo akumuopa Iye; Kuti m'dziko mwathu mukhale ulemu.