Psalms 86:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Inu ndinu wamkulu, mumachita zinthu zodabwitsa, Inu nokha ndinu Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Inu ndinu wamkulu, ndi wakuchita zodabwitsa; Inu ndinu Mulungu, nokhanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndinu wamkulu ndipo mumachita zodabwitsa; Inu nokha ndiye Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Inu ndinu wamkulu, ndi wakucita zodabwiza; Inu ndinu Mulungu, nokhanu.