Psalms 86:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Phunzitseni njira zanu, Inu Chauta, kuti ndiziyenda m'zoona zanu. Mundipatse mtima wosagaŵikana, kuti ndiziwopa dzina lanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundionetse njira yanu, Yehova; ndidzayenda m'choonadi chanu, muumbe mtima wanga ukhale umodzi kuti uliope dzina lanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiphunzitseni njira yanu Yehova, ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu; patseni mtima wosagawikana kuti ndilemekeze dzina lanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundionetse njira yanu, Yehova; ndidzayenda m'coonadi canu: Muumbe mtima wanga ukhale umodzi kuti uliope dzina lanu.