Psalms 86:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Ambuye, Mulungu wanga, ndikukuthokozani ndi mtima wanga wonse, ndidzalemekeza ukulu wanu mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakuyamikani, Ambuye, Mulungu wanga, ndi mtima wanga wonse; ndipo ndidzalemekeza dzina lanu nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakutamandani Ambuye Mulungu wanga, ndi mtima wanga wonse; ndidzalemekeza dzina lanu kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakuyamikani, Ambuye, Mulungu wanga, ndi mtima wanga wonse; Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu nthawi zonse.