Psalms 86:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja chikondi chanu chosasinthika kwa ine nchachikulu, Mwandipulumutsa ku malo akuya a anthu akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chifundo chanu cha pa ine nchachikulu; ndipo munalanditsa moyo wanga kunsi kwa manda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti chikondi chanu nʼchachikulu kwa ine; mwandipulumutsa ku malo ozama a manda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti cifundo canu ca pa ine ncacikuru; Ndipo munalanditsa moyo wanga kunsi kwa manda.