Psalms 86:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, anthu achipongwe andiwukira. Anthu opanda chifundo akufunafuna moyo wanga ndipo sasamala za Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu, odzikuza andiukira, ndi msonkhano wa anthu oopsa afuna moyo wanga, ndipo sanaike Inu pamaso pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Mulungu wanga, anthu odzikuza akundithira nkhondo; anthu ankhanza akufuna kundipha, amene salabadira za Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu, odzikuza andiukira, Ndi msonkhano wa anthu oopsa afuna moyo wanga, Ndipo sanaika Inu pamaso pao.