Psalms 86:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundiyang'ane ndipo mundichitire chifundo. Mundipatse mphamvu zanu ine mtumiki wanu, mundipulumutse ine mwana wa mdzakazi wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundibwerere ine, ndi kundichitira chifundo; mpatseni mtumiki wanu mphamvu yanu, ndipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tembenukirani kwa ine ndipo ndichitireni chifundo; perekani mphamvu zanu kwa mtumiki wanu ndipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundibwerere ine, ndi kundicitira cifundo; Mpatseni mtumiki wanu mphamvu yanu, Ndipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu.