Psalms 86:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundiwonetse chizindikiro chakuti mumandikomera mtima, kuti odana nane achite manyazi. Adzaona kuti Inu Chauta mwandithandiza ndi kundilimbitsa mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundichitire chizindikiro choti chabwino; kuti ondida achione, nachite manyazi, popeza Inu, Yehova, munandithandiza ndi kundisangalatsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mundionetse chizindikiro cha ubwino wanu kuti adani achione ndi kuchititsidwa manyazi, pakuti Yehova mwandithandiza ndi kunditonthoza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundicitire cizindikilo coti cabwino; Kuti ondida acione, nacite manyazi, Popeza Inu, Yehova, munandithandiza ndi kundisangalatsa,