Psalms 86:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sangalatsani mtima wa ine mtumiki wanu, pakuti ndikupereka mtima wanga kwa Inu Ambuye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kondwetsani moyo wa mtumiki wanu; pakuti ndikwezera moyo wanga kwa Inu, Ambuye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bweretsani chimwemwe kwa mtumiki wanu, Ambuye, pakuti ndimadalira Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kondwetsani moyo wa mtumiki wanu; Pakuti ndikwezera moyo wanga kwa Inu, Ambuye.