Psalms 86:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakati pa milungu palibe ndi mmodzi yemwe wolingana nanu, Inu Ambuye, palibe ntchito zolingana ndi ntchito zanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakati pa milungu palibe wina wonga Inu, Ambuye; ndipo palibe ntchito zonga zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakati pa milungu palibe wina wofanana nanu Ambuye; palibe ntchito zolingana ndi ntchito zanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakati pa milungu palibe wina wonga Inu, Ambuye; Ndipo palibe nchito zonga zanu.