Psalms 87:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe mzinda wa Mulungu, anthu amakamba zambiri zotamanda iwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzi wa Mulungu, inu, akunenerani zakukulemekezani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za ulemerero wako zimakambidwa, Iwe mzinda wa Mulungu: Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzi wa Mulungu, inu, Akunenerani zakukulemekezani.