Psalms 87:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ponena za Ziyoni adzati, “Onse adabadwira kumeneko,” chifukwa Wopambanazonse mwini wake ndiye amene adzaulimbitsa mzindawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzanena za Ziyoni, uyu ndi uyo anabadwa m'mwemo; ndipo Wam'mwambamwamba ndiye adzaukhazikitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithudi, za Ziyoni adzanena kuti, “Uyu ndi uyo anabadwira mwa iye, ndipo Wammwambamwamba adzakhazikitsa iyeyo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzanena za Ziyoni, Uyu ndi uyo anabadwa m'mwemo; Ndipo Wam'mwambamwamba ndiye aclzaukhazikitsa.