Psalms 88:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi zodabwitsa mumachitira anthu akufa? Kodi iwowo nkuuka kuti akutamandeni?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mudzachitira akufa zodabwitsa? Kodi adzaukanso otisiyawo, ndi kukulemekezani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mumaonetsa zozizwitsa zanu kwa anthu akufa? Kodi iwo amene afa amaukanso ndi kutamanda Inu? Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mudzacitira akufa zodabwiza? Kodi adzaukanso otisiyawo, ndi kukulemekezani?