Psalms 88:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi zodabwitsa zanu zimadziŵika mu mdima? Ndani angadziŵe za chithandizo chanu chopulumutsa m'dziko la anthu oiŵalika?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zodabwitsa zanu zidadziwika mumdima kodi, ndi chilungamo chanu m'dziko la chiiwaliko?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi zozizwitsa zanu zimadziwika ku malo a mdima, kapena ntchito zanu zolungama ku dziko la anthu oyiwalika?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zodabwiza zanu zidzadziwika mumdima kodi, Ndi cilungamo canu m'dziko la ciiwaliko?