Psalms 88:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine ndimalirira Inu Chauta, m'maŵa pemphero langa limakafika kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndinafuulira kwa Inu, Yehova, ndipo pemphero langa lifika kwa Inu mamawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, Ine ndimalirira thandizo; mmawa mapemphero anga amafika pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndinapfuulira kwa Inu, Yehova, Ndipo pemphero langa likumika Inu mamawa.