Psalms 88:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuyambira ubwana wanga mpaka kukula, ndakhala ndikupirira zilango zanu pozunzika mpaka pafupi kufa, tsopano ndatheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wozunzika ine ndi wofuna kufa kuyambira ubwana wanga; posenza zoopsa zanu, ndithedwa nzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuyambira ubwana wanga ndakhala ndikuzunzika pafupi kufa; ndakhala ndikuchita mantha ndipo ndine wothedwa nzeru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wozunzika ine ndi wofuna kufa kuyambira ubwana wanga; Posenza zoopsa zanu, ndithedwa nzeru.