Psalms 88:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkwiyo wanu wandimiza, moyo wanga waonongekeratu ndi ukali wanu woopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuzaza kwanu kwandimiza; zoopsa zanu zinandiononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukali wanu wandimiza; zoopsa zanu zandiwononga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuzaza kwanu kwandimiza; Zoopsa zanu zinandiononga,