Psalms 88:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti mtima wanga ndi wodzaza ndi mavuto, moyo wanga ukuyandikira ku malo a anthu akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mzimu wanga wadzala nao mavuto, ndi moyo wanga wayandikira kumanda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndili ndi mavuto ambiri ndipo moyo wanga ukuyandikira ku manda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mzimu wanga wadzala nao mabvuto, Ndi moyo wanga wayandikira kumanda.