Psalms 88:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikuŵerengedwa pamodzi ndi anthu otsikira ku manda. Ndasanduka munthu wopanda mphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandiwerenga pamodzi nao otsikira kudzenje; ndakhala ngati munthu wopanda mphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikuwerengedwa pamodzi ndi iwo amene akutsikira ku dzenje; ndine munthu wopanda mphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandiwerenga pamodzi nao otsikira kudzenje; Ndakhala ngati munthu wopanda mphamvu: