Psalms 88:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwandiika pansi penipeni pa dzenje m'malo akuya a mdima wandiweyani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munandiika kunsi kwa dzenje, kuli mdima, kozama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwandiyika pansi pa dzenje penipeni, mʼmalo akuya a mdima waukulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munandiika kunsi kwa dzenje, Kuti mdima, kozama.