Psalms 88:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkwiyo wanu ukundipsinja, mukundimiza ndi mafunde anu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkwiyo wanu utsamira pa ine, ndipo munandizunza ine ndi mafunde anu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukali wanu ukundipsinja kwambiri, mwandiopseza kwambiri ndi mafunde anu onse. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mkwiyo wanu utsamira pa ine, Ndipo munandizunza ine ndi mafunde anu onse.