Psalms 88:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwachititsa kuti anzanga azindithaŵa, mwandisandutsa chinthu choŵanyansa. Ndatsekerezedwa kotero kuti sindingathe kuthaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munandisiyanitsira wodziwana nane kutali; munandiika ndiwakhalire chonyansa. Ananditsekereza, osakhoza kutuluka ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwandichotsa pakati pa abwenzi anga enieni ndipo mwachititsa kuti ndikhale chonyansa kwa iwo. Ndatsekerezedwa ndipo sindingathe kuthawa;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munandisiyanitsira wodziwana nane kutali; Munandiika ndiwakhalire conyansa: Ananditsekereza osakhoza kuturuka ine.