Psalms 88:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maso mwanga mwada ndi chisoni. Tsiku ndi tsiku ndimakuitanani, Inu Chauta, Ndimakweza manja anga kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Diso langa lapuwala chifukwa cha kuzunzika kwanga: Ndimaitana Inu, Yehova, tsiku lonse; nditambalitsira manja anga kwa Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
maso anga ada ndi chisoni. Ndimayitana Inu Yehova tsiku lililonse; ndimakweza manja anga kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Diso langa lapuwala cifukwa ca kuzunzika kwanga: Ndimaitana Inu, Yehova, tsiku lonse; Nditambalitsira manja anga kwa Inu.