Psalms 89:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, ndidzaimba mosalekeza nyimbo yotamanda chikondi chanu chosasinthika. Ndidzalalika ndi pakamwa panga za kukhulupirika kwanu ku mibadwo yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chilangizo cha Etani Mwezara. Ndidzaimbira zachifundo za Yehova nthawi yonse, pakamwa panga ndidzadziwitsira chikhulupiriko chanu ku mibadwomibadwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndakatulo ya Etani, wa banja la Ezara. Ndidzayimba za chikondi chachikulu cha Yehova kwamuyaya; ndi pakamwa panga ndidzachititsa kuti kukhulupirika kwanu kudziwike ku mibado yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzayimbira zacifundo za Yehova nthawi yonse: Pakamwa panga ndidzadziwitsira cikhulupiriko canu ku mibadwo mibadwo.