Psalms 89:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudatswanya chilombo cha m'nyanja ndi kuchisandutsa mtembo. Mudabalalitsa adani anu ndi mkono wanu wamphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudathyola Rahabu, monga munthu wophedwa; munabalalitsa adani anu ndi mkono wa mphamvu yanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munaphwanya Rahabe monga munthu wophedwa; ndi dzanja lanu lamphamvu munabalalitsa adani anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudathyola Rahabu, monga munthu wophedwa; Munabalalitsa adani anu ndi mkono wa mphamvu yanu.