Psalms 89:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu muli ndi mphamvu zonse. Dzanja lanu ndi lamphamvu kwambiri, dzanja lanu lamanja ndi lopambana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muli nao mkono wanu wolimba; m'dzanja mwanu muli mphamvu, dzanja lamanja lanu nlokwezeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkono wanu ndi wamphamvu; dzanja lanu ndi lamphamvu, dzanja lanu lamanja ndi lopambana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muli nao mkono wanu wolimba; M'dzanja mwanu muli mphamvu, dzanja lamanja lanu nlokwezeka.