Psalms 89:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngodala anthu amene mumaŵaphunzitsa kuimba nyimbo zachikondwerero, amene amayenda m'chikondi chanu, Inu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Odala anthu odziwa liu la lipenga; ayenda m'kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi odala amene aphunzira kuyamika Inu, amene amayenda mʼkuwunika kwa nkhope yanu Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Odala anthu odziwa liu la lipenga; Ayenda m'kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.