Psalms 89:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kotero kuti dzanja langa lidzamchirikiza mpaka muyaya, mkono wanganso udzamulimbitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene dzanja langa lidzakhazikika naye; inde mkono wanga udzalimbitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzanja langa lidzamuchirikiza; zoonadi, mkono wanga udzamupatsa mphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene dzanja langa lidzakhazikika naye; Inde mkono wanga udzalimbitsa.