Psalms 89:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Adani sadzampambana, anthu oipa sadzamtsitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mdani sadzamuumira mtima; ndi mwana wa chisalungamo sadzamzunza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani sadzamulamula kuti apereke msonkho; anthu oyipa sadzamusautsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mdani sadzamuumira mtima; Ndi mwana wa cisalungamo sadzamzunza.