Psalms 89:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kukhulupirika ndiponso chikondi changa chosasinthika zidzakhala naye, ndidzalimbitsa mphamvu zake, kuti mbiri yanga isungike.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma chikhulupiriko changa ndi chifundo changa zidzakhala naye; ndipo nyanga yake idzakwezeka m'dzina langa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikondi changa chokhulupirika chidzakhala naye, ndipo kudzera mʼdzina langa nyanga yake idzakwezedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma cikhulupiriko canga ndi cifundo canga zidzakhala naye; Ndipo nyanga yace idzakwezeka m'dzina langa.