Psalms 89:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuza ufumu wake kuchokera ku Nyanja Yaikulu mpaka kukafika ku mtsinje wa Yufurate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzaika dzanja lake panyanja, ndi dzanja lamanja lake pamitsinje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzayika dzanja lake pa nyanja, dzanja lake lamanja pa mitsinje.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzaika dzanja lace panyanja, Ndi dzanja lamanja lace pamitsinje.