Psalms 89:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu ndidzamsandutsa mwana wanga wachisamba, adzakhala wopambana mafumu a dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde ndidzamuyesa mwana wanga woyamba, womveka wa mafumu a pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzamuyika kuti akhale mwana wanga woyamba kubadwa; wokwezedwa kwambiri pakati pa mafumu a dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde ndidzamuyesa mwana wanga woyamba, Womveka wa mafumu a pa dziko lapansi.