Psalms 89:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakhazikitsa zidzukulu zake pa mpando wachifumu, mpaka muyaya, ndipo ufumu wake udzakhala waukulu ngati mlengalenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakhalitsanso mbeu yake chikhalire, ndi mpando wachifumu wake ngati masiku a m'mwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzakhazikitsa zidzukulu zake mpaka muyaya, mpando wake waufumu ngati masiku a miyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakhalitsanso mbeu yace cikhalire, Ndi mpando wacifumu wace ngati masiku a m'mwamba.