Psalms 89:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwanena kuti, “Ndachita chipangano ndi wosankhidwa wanga, ndalumbira kwa Davide mtumiki wanga kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinachita chipangano ndi wosankhika wanga, ndinalumbirira Davide mtumiki wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munati, “Ndachita pangano ndi wosankhidwa wanga, ndalumbira kwa Davide mtumiki wanga kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinacita cipangano ndi wosankhika wanga, Ndinalumbirira Davide mtumiki wanga: