Psalms 89:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma ngati ana ake asiya lamulo langa, ndipo satsata malangizo anga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana ake akataya chilamulo changa, osayenda m'maweruzo anga,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati ana ake adzataya lamulo langa ndi kusatsatira malangizo anga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana ace akataya cilamulo canga, Osayenda m'maweruzo anga: