Psalms 89:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Sindidzaswa chipangano changa, kapena kusintha mau otuluka pakamwa panga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sindidzaipsa chipangano changa, kapena kusintha mau otuluka m'milomo yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sindidzaswa pangano langa kapena kusintha zimene milomo yanga yayankhula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sindidzaipsa cipangano canga, Kapena kusintha mau oturuka m'milomo yanga.