Psalms 89:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zidzukulu zake sizidzatha mpaka muyaya, mpando wake wachifumu udzakhalapo nthaŵi zonse, monga m'mene likhalira dzuŵa pamaso panga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbeu yake idzakhala kunthawi yonse, ndi mpando wachifumu wake ngati dzuwa pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti zidzukulu zake zidzakhale kwamuyaya ndipo mpando wake waufumu udzakhazikika pamaso panga ngati dzuwa;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbeu yace idzakhala ku nthawi yonse, Ndi mpando wacifumu wace ngati dzuwa pamaso panga.