Psalms 89:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ufumu wake udzakhazikika mpaka muyaya ngati mwezi, mboni yanga yokhulupirika mu mlengalenga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzakhazikika ngati mwezi kunthawi yonse, ndi ngati mboni yokhulupirika kuthambo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
udzakhazikika kwamuyaya monga mwezi, mboni yokhulupirika mʼmitambo. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzakhazikika ngati mwezi ku nthawi yonse, Ndi ngati mboni yokhulupirika kuthambo.