Psalms 89:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsopano Inu mwamtaya ndi kumkana wodzozedwa wanu, mwamkwiyira kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Inu munamtaya, nimunamkaniza, munakwiya naye wodzozedwa wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma tsopano Inu mwamukana, mwamutaya, mwamukwiyira kwambiri wodzozedwa wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Inu munamtaya, nimunamkaniza, Munakwiya naye wodzozedwa wanu.