Psalms 89:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwakana chipangano chanu ndi mtumiki wanu, mwadetsa m'fumbi chisoti chake chaufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munakaniza chipangano cha mtumiki wanu; munaipsa korona wake ndi kumponya pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwakana pangano ndi mtumiki wanu ndipo mwadetsa mʼfumbi chipewa chake chaufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munakaniza cipangano ca mtumiki wanu; Munaipsa korona wace ndi kumponya pansi,